Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 26:23 - Buku Lopatulika

23 Ana aamuna a Isakara monga mwa mabanja ao ndiwo: Tola, ndiye kholo la banja la Atola; Puva, ndiye kholo la banja la Apuni;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Ana amuna a Isakara monga mwa mabanja ao ndiwo: Tola, ndiye kholo la banja la Atola; Puva, ndiye kholo la banja la Apuni;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Potsata mabanja ao ana aamuna a Isakara anali aŵa: Tola anali kholo la banja la Atola. Puva anali kholo la banja la Apuva.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Zidzukulu za Isakara monga mwa mafuko awo zinali izi: kuchokera mwa Tola, fuko la Atola; kuchokera mwa Puwa, fuko la Apuwa;

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:23
6 Mawu Ofanana  

Ndi ana aamuna a Isakara: Tola ndi Puva, ndi Iyobu, ndi Simironi.


Ana a Isakara ndiwo Tola, ndi Puwa, Yasubu ndi Simironi; anai.


A ana a Isakara, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;


Ndipo iwo akumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a fuko la Isakara; ndipo kalonga wa ana a Isakara ndiye Netanele mwana wa Zuwara.


Yasubu, ndiye kholo la banja la Ayasubu; Simironi, ndiye kholo la banja la Asimironi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa