Numeri 26:24 - Buku Lopatulika24 Yasubu, ndiye kholo la banja la Ayasubu; Simironi, ndiye kholo la banja la Asimironi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Yasubu, ndiye kholo la banja la Ayasubu; Simironi, ndiye kholo la banja la Asimironi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Yasubu anali kholo la banja la Ayasubu. Simeoni anali kholo la banja la Asimeoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 kuchokera mwa Yasubu, fuko la Ayasubu. Kuchokera mwa Simironi, fuko la Asimironi. Onani mutuwo |