Numeri 26:25 - Buku Lopatulika25 Iwo ndiwo mabanja a Isakara monga mwa owerengedwa ao; zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Iwo ndiwo mabanja a Isakara monga mwa owerengedwa ao; zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Ameneŵa, anthu okwanira 64,300, ndiwo anali a m'mabanja a Isakara, amene adaŵerengedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Awa ndi amene anali a fuko la Isakara. Amene anawerengedwa analipo 64,300. Onani mutuwo |