Numeri 26:26 - Buku Lopatulika26 Ana aamuna a Zebuloni monga mwa mabanja ao ndiwo: Seredi, ndiye kholo la banja la Aseredi; Eloni, ndiye kholo la banja la Aeloni; Yaleele, ndiye kholo la banja la Ayaleele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ana amuna a Zebuloni monga mwa mabanja ao ndiwo: Seredi, ndiye kholo la banja la Aseredi; Eloni, ndiye kholo la banja la Aeloni; Yaleele, ndiye kholo la banja la Ayaleele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Potsata mabanja ao ana aamuna a Zebuloni anali aŵa: Seredi anali kholo la banja la Aseredi. Eloni anali kholo la banja la Aeloni. Yaleele anali kholo la banja la Ayaleele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Zidzukulu za Zebuloni mwa mafuko awo zinali izi: kuchokera mwa Seredi, fuko la Aseredi; kuchokera mwa Eloni, fuko la Aeloni; kuchokera mwa Yahaleeli, fuko la Ayahaleeli. Onani mutuwo |