Numeri 26:27 - Buku Lopatulika27 Iwo ndiwo mabanja a Zebuloni monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu mazana asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Iwo ndiwo mabanja a Zebuloni monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu mazana asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Ameneŵa, anthu okwanira 60,500, ndiwo anali a m'mabanja a Zebuloni, amene adaŵerengedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Awa ndiwo anali mafuko a Zebuloni. Amene anawerengedwa analipo 60,500. Onani mutuwo |