Numeri 26:28 - Buku Lopatulika28 Ana aamuna a Yosefe monga mwa mabanja ao ndiwo: Manase ndi Efuremu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ana amuna a Yosefe monga mwa mabanja ao ndiwo: Manase ndi Efuremu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Potsata mabanja ao ana aamuna a Yosefe anali aŵa: Manase ndi Efuremu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Zidzukulu za Yosefe mwa mafuko awo kupyolera mwa Manase ndi Efereimu zinali izi: Onani mutuwo |