Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 26:21 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Zidzukulu za Perezi zinali izi: kuchokera mwa Hezironi, fuko la Ahezironi; kuchokera mwa Hamuli, fuko la Ahamuli.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

21 Ndipo ana a Perezi ndiwo: Hezironi, ndiye kholo la banja la Ahezironi; Hamuli, ndiye kholo la banja la Ahamuli.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Ndipo ana a Perezi ndiwo: Hezironi, ndiye kholo la banja la Ahezironi; Hamuli, ndiye kholo la banja la Ahamuli.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Tsono ana aamuna a Perezi anali aŵa: Hezironi anali kholo la banja la Ahezironi. Hamuli anali kholo la banja la Ahamuli.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:21
7 Mawu Ofanana  

Ana aamuna a Yuda ndi awa: Eri, Onani, Sela, Perezi ndi Zera. Koma Eri ndi Onani anamwalira mʼdziko la Kanaani. Ana a Perezi anali Hezironi ndi Hamuli.


Ana a Perezi anali awa: Hezironi ndi Hamuli.


Zidzukulu za Yuda monga mwa mafuko awo zinali izi: kuchokera mwa Sela, fuko la Asera; kuchokera mwa Perezi, fuko la Aperezi; kuchokera mwa Zera, mbumba ya Zera.


Awa ndiwo anali mafuko a Yuda. Amene anawerenga analipo 76,500.


kuchokera mwa Hezironi, fuko la Ahezironi; kuchokera mwa Karimi, fuko la Akarimi.


Awa anali mafuko a Rubeni: onse amene anawerengedwa analipo 43,730.


Yuda anabereka Perezi ndi Zara, amene amayi awo anali Tamara. Perezi anabereka Hezironi, Hezironi anabereka Aramu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa