Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 26:7 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Awa anali mafuko a Rubeni: onse amene anawerengedwa analipo 43,730.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

7 Iwo ndiwo mabanja a Arubeni; owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zitatu kudza mazana asanu ndi awiri mphambu makumi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Iwo ndiwo mabanja a Arubeni; owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi anai mphambu zitatu kudza mazana asanu ndi awiri mphambu makumi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Ameneŵa, anthu okwanira 43,730, ndiwo anali a m'mabanja a Rubeni, amene adaŵerengedwa.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:7
7 Mawu Ofanana  

Ana aamuna a Rubeni ndi awa: Hanoki, Palu, Hezironi ndi Karimi.


Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Rubeni chinali 46,500.


Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 46,500.


Utatha mliri Yehova anati kwa Mose ndi Eliezara mwana wa Aaroni,


Zidzukulu za Perezi zinali izi: kuchokera mwa Hezironi, fuko la Ahezironi; kuchokera mwa Hamuli, fuko la Ahamuli.


kuchokera mwa Hezironi, fuko la Ahezironi; kuchokera mwa Karimi, fuko la Akarimi.


Mwana wa Palu anali Eliabu,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa