Numeri 1:21 - Buku Lopatulika21 owerengedwa ao a fuko la Rubeni, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu ndi chimodzi kudza mazana asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 owerengedwa ao a fuko la Rubeni, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu ndi chimodzi kudza mazana asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Rubeni, adapezeka kuti ali 46,500. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Rubeni chinali 46,500. Onani mutuwo |