Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 1:21 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Rubeni chinali 46,500.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

21 owerengedwa ao a fuko la Rubeni, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu ndi chimodzi kudza mazana asanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 owerengedwa ao a fuko la Rubeni, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu ndi chimodzi kudza mazana asanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Rubeni, adapezeka kuti ali 46,500.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:21
4 Mawu Ofanana  

Kuchokera mwa ana a Rubeni, mwana wamwamuna woyamba wa Israeli: Amuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali, anawalemba mayina awo, mmodzimmodzi monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.


Kuchokera mwa zidzukulu za Simeoni: Amuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali anawalemba mayina awo, mmodzimmodzi monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.


Awa anali mafuko a Rubeni: onse amene anawerengedwa analipo 43,730.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa