Numeri 26:6 - Buku Lopatulika6 Hezironi, ndiye kholo la banja la Ahezironi; Karimi, ndiye kholo la banja la Akarimi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Hezironi, ndiye kholo la banja la Ahezironi; Karimi, ndiye kholo la banja la Akarimi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Hezironi anali kholo la banja la Ahezironi. Karimi anali kholo la banja la Akarimi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 kuchokera mwa Hezironi, fuko la Ahezironi; kuchokera mwa Karimi, fuko la Akarimi. Onani mutuwo |