Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 26:6 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 kuchokera mwa Hezironi, fuko la Ahezironi; kuchokera mwa Karimi, fuko la Akarimi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

6 Hezironi, ndiye kholo la banja la Ahezironi; Karimi, ndiye kholo la banja la Akarimi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Hezironi, ndiye kholo la banja la Ahezironi; Karimi, ndiye kholo la banja la Akarimi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Hezironi anali kholo la banja la Ahezironi. Karimi anali kholo la banja la Akarimi.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:6
5 Mawu Ofanana  

Nthawi yakupha ndi nthawi yochiritsa, nthawi yogwetsa ndi nthawi yomanga.


Koma ana anu amene mukunena kuti adzatengedwa ngati katundu wolanda ku nkhondo, Ine ndidzawalowetsa kuti akasangalale mʼdziko limene munalikana.


Zidzukulu za Perezi zinali izi: kuchokera mwa Hezironi, fuko la Ahezironi; kuchokera mwa Hamuli, fuko la Ahamuli.


Zidzukulu za Rubeni, mwana woyamba wamwamuna wa Israeli, zinali izi: kuchokera mwa Hanoki, fuko la Ahanoki; kuchokera mwa Palu, fuko la Apalu;


Awa anali mafuko a Rubeni: onse amene anawerengedwa analipo 43,730.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa