Numeri 26:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo kunali, utatha mliriwo, Yehova ananena ndi Mose ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, nati, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo kunali, utatha mliriwo, Yehova ananena ndi Mose ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, nati, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Utatha mliriwo, Chauta adauza Mose ndi Eleazara, mwana wa wansembe Aroni, kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Utatha mliri Yehova anati kwa Mose ndi Eliezara mwana wa Aaroni, Onani mutuwo |