Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 26:1 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Utatha mliri Yehova anati kwa Mose ndi Eliezara mwana wa Aaroni,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

1 Ndipo kunali, utatha mliriwo, Yehova ananena ndi Mose ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, nati,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndipo kunali, utatha mliriwo, Yehova ananena ndi Mose ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, nati,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Utatha mliriwo, Chauta adauza Mose ndi Eleazara, mwana wa wansembe Aroni, kuti,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:1
3 Mawu Ofanana  

monga momwe Yehova analamulira Mose. Motero iyeyo anawawerenga mʼchipululu cha Sinai:


chifukwa ankakuonani inu ngati adani awo pamene anakupusitsani pa nkhani ya ku Peori, ndiponso za mlongo wawo Kozibi, mwana wamkazi wa mtsogoleri wa Amidiyani, mkazi yemwe anaphedwa pamene mliri unabwera chifukwa cha zimene zinachitika ku Peori.”


Pa mliriwo, anthu okwana 24,000 anafa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa