Numeri 25:18 - Buku Lopatulika18 popeza akusautsani ndi manyengo ao amene anakunyengani nao; m'chija cha Peori, ndi cha Kozibi, mwana wamkazi wa kalonga wa ku Midiyani, mlongo wao, amene adamupha tsiku la mliri, m'chija cha Peori. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 popeza akusautsani ndi manyengo ao amene anakunyengani nao; m'chija cha Peori, ndi cha Kozibi, mwana wamkazi wa kalonga wa ku Midiyani, mlongo wao, amene adamupha tsiku la mliri, m'chija cha Peori. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 chifukwa choti adakuchitani zachabe pokunyengani ku Peori, ndiponso chifukwa cha nkhani ya mlongo wao Kozibi, mwana wamkazi wa mfumu ya ku Midiyani, amene adaphedwa pa nthaŵi ya mliri chifukwa cha zochitika ku Peori zija.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 chifukwa ankakuonani inu ngati adani awo pamene anakupusitsani pa nkhani ya ku Peori, ndiponso za mlongo wawo Kozibi, mwana wamkazi wa mtsogoleri wa Amidiyani, mkazi yemwe anaphedwa pamene mliri unabwera chifukwa cha zimene zinachitika ku Peori.” Onani mutuwo |