Masalimo 9:3 - Buku Lopatulika Pobwerera m'mbuyo adani anga, akhumudwa naonongeka pankhope panu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Pobwerera m'mbuyo adani anga, akhumudwa naonongeka pankhope panu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mukangofika, adani anga amathaŵa, amaphunthwa ndi kufa pamaso panu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Adani anga amathawa, iwo amapunthwa ndi kuwonongedwa pamaso panu. |
Popeza udati, Inu Yehova, ndinu pothawirapo panga! Udaika Wam'mwambamwamba chokhalamo chako;
Pamene Inu munachita zinthu zoopsa, zimene ife sitinayang'anira, Inu munatsika, mapiri anagwedezeka pamaso panu.
amene adzamva chilango, ndicho chionongeko chosatha chowasiyanitsa kunkhope ya Ambuye, ndi kuulemerero wa mphamvu yake,
Ndipo ndinaona, mpando wachifumu waukulu woyera, ndi Iye wakukhalapo, amene dziko ndi m'mwamba zinathawa pamaso pake, ndipo sanapezedwe malo ao.