Masalimo 91:9 - Buku Lopatulika9 Popeza udati, Inu Yehova, ndinu pothawirapo panga! Udaika Wam'mwambamwamba chokhalamo chako; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Popeza udati, Inu Yehova, ndinu pothawirapo panga! Udaika Wam'mwambamwamba chokhalamo chako; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Chifukwa chakuti wavomera Chauta kuti akhale malo ako othaŵirako, wavomera Wopambanazonse kuti akhale malo ako okhalamo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pakuti wasankha Wammwambamwamba kukhala malo ako okhalamo; wavomera Yehova kukhala kothawira kwako. Onani mutuwo |