Masalimo 91:10 - Buku Lopatulika10 palibe choipa chidzakugwera, ndipo cholanga sichidzayandikiza hema wako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 palibe choipa chidzakugwera, ndipo cholanga sichidzayandikiza hema wako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 zoipa sizidzakugwera, zoopsa sizidzafika pafupi ndi nyumba yako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Choncho palibe choyipa chimene chidzakugwera, zoopsa sizidzafika pafupi ndi tenti yako. Onani mutuwo |