Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 80:16 - Buku Lopatulika

16 Unapserera ndi moto, unadulidwa; aonongeka pa kudzudzula kwa nkhope yanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Unapserera ndi moto, unadulidwa; aonongeka pa kudzudzula kwa nkhope yanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Adani athu autentha, augwetsa pansi. Ayang'aneni iwowo mokwiya ndi kuŵaononga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Mpesa wanu wadulidwa ndi kutenthedwa ndi moto; pakudzudzula kwanu anthu anu awonongeka.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 80:16
8 Mawu Ofanana  

Pamene mulanga munthu ndi zomdzudzula chifukwa cha mphulupulu, mukanganula kukongola kwake monga mumachita ndi njenjete. Indedi, munthu aliyense ali chabe.


Yehova, mudzakwiya nthawi zonse kufikira liti? Nidzatentha nsanje yanu ngati moto?


Pakuti tionongeka mu mkwiyo wanu; ndipo m'kuzaza kwanu tiopsedwa.


Ponyala nthambi zake zidzathyoledwa; akazi adzafika, nazitentha ndi moto, pakuti ali anthu opanda nzeru; chifukwa chake Iye amene anawalenga sadzawachitira chisoni, ndi Iye amene anawaumba sadzawakomera mtima.


Ngati wina sakhala mwa Ine, watayika kunja monga nthambi, nafota; ndipo azisonkhanitsa nazitaya kumoto, nazitentha.


amene adzamva chilango, ndicho chionongeko chosatha chowasiyanitsa kunkhope ya Ambuye, ndi kuulemerero wa mphamvu yake,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa