Masalimo 9:4 - Buku Lopatulika4 Pakuti mwandiweruzira mlandu wanga; mwakhala pa mpando wachifumu, woweruza wolungama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pakuti mwandiweruzira mlandu wanga; mwakhala pa mpando wachifumu, woweruza wolungama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Inu mwatsimikiza kusalakwa kwanga. Mwakhala pa mpando woweruza, mwagamula kuti ndine wosapalamula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Pakuti Inu mwatsimikiza za kulungama kwanga ndi mlandu wanga; Inu mwakhala pa mpando wanu waufumu, kuweruza mwachilungamo. Onani mutuwo |