Masalimo 9:3 - Buku Lopatulika3 Pobwerera m'mbuyo adani anga, akhumudwa naonongeka pankhope panu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pobwerera m'mbuyo adani anga, akhumudwa naonongeka pankhope panu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mukangofika, adani anga amathaŵa, amaphunthwa ndi kufa pamaso panu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Adani anga amathawa, iwo amapunthwa ndi kuwonongedwa pamaso panu. Onani mutuwo |