Masalimo 76:7 - Buku Lopatulika7 Inu ndinu woopsa; ndipo utauka mkwiyo wanu adzakhala chilili ndani pamaso panu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Inu ndinu woopsa; ndipo utauka mkwiyo wanu adzakhala chilili ndani pamaso panu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Zoonadi, Inu ndinu woopsa. Angathe kuima pamaso panu ndani pamene mkwiyo wanu wayaka? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Inu nokha ndiye muyenera kuopedwa. Angathe kuyima pamaso panu ndani mukakwiya? Onani mutuwo |