Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 92:2 - Buku Lopatulika

2 Kuonetsera chifundo chanu mamawa, ndi chikhulupiriko chanu usiku uliwonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Kuonetsera chifundo chanu mamawa, ndi chikhulupiriko chanu usiku uliwonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Nkwabwino m'maŵa kulalika za chikondi chanu chosasinthika, ndipo usiku kusimba za kukhulupirika kwanu,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Kulengeza chikondi chanu mmawa, ndi kukhulupirika kwanu nthawi ya usiku,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 92:2
14 Mawu Ofanana  

Ndipo Davide ndi akazembe a gulu la nkhondo anapatulira utumikiwo ena a ana a Asafu, ndi a Hemani, ndi a Yedutuni, anenere ndi azeze, ndi zisakasa, ndi nsanje; ndi chiwerengo cha antchito monga mwa kutumikira kwao ndicho:


Koma palibe anganene, Ali kuti Mulungu Mlengi wanga, wakupatsa nyimbo usiku;


Ndidzaimba zachifundo ndi chiweruzo; ndidzaimba zakukulemekezani Inu, Yehova.


Masiku onse ndidzakuyamikani; ndi kulemekeza dzina lanu kunthawi za nthawi.


Aleluya; Pakuti kuimbira zomlemekeza Mulungu wathu nkokoma; pakuti chikondweretsa ichi, chilemekezo chiyenera.


Koma usana Yehova adzalamulira chifundo chake, ndipo usiku nyimbo yake idzakhala ndi ine. Inde pemphero la kwa Mulungu wa moyo wanga.


Pakamwa panga padzafotokozera chilungamo chanu, ndi chipulumutso chanu tsiku lonse; pakuti sindidziwa mawerengedwe ake.


Tsiku la nsautso yanga ndinafuna Ambuye. Dzanja langa linatambalika usiku, losaleka; mtima wanga unakana kutonthozedwa.


Pobwerera m'mbuyo adani anga, akhumudwa naonongeka pankhope panu.


Ndidzatchula zachifundo chake cha Yehova, ndi matamando a Yehova, monga mwa zonse zimene Yehova wapereka kwa ife; ndi ubwino wake waukulu kwa banja la Israele, umene Iye wapereka kwa iwo, monga mwa chifundo chake, ndi monga mwa ntchito zochuluka za chikondi chake.


Chifukwa chilamulo chinapatsidwa mwa Mose; chisomo ndi choonadi zinadza mwa Yesu Khristu.


Koma ngati pakati pa usiku, Paulo ndi Silasi analinkupemphera, naimbira Mulungu nyimbo, ndipo a m'ndendemo analinkuwamva;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa