Ndipo masiku a Saulo anagwirana nkhondo ndi Ahagiri, amene adagwa ndi dzanja lao; ndipo anakhala m'mahema mwao kum'mawa konse kwa Giliyadi.
Masalimo 83:6 - Buku Lopatulika Mahema a Edomu ndi a Aismaele; Mowabu ndi Ahagiri; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mahema a Edomu ndi a Aismaele; Mowabu ndi Ahagiri; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa anthu okhala m'mahema a Aedomu ndi Aismaele, Amowabu ndi Ahagara, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Matenti a Edomu ndi Aismaeli, Mowabu ndi Ahagiri, |
Ndipo masiku a Saulo anagwirana nkhondo ndi Ahagiri, amene adagwa ndi dzanja lao; ndipo anakhala m'mahema mwao kum'mawa konse kwa Giliyadi.
Ndipo zitatha izi, kunachitika kuti ana a Mowabu, ndi ana a Amoni, ndi ena pamodzi ndi Aamoni, anadza kuyambana nkhondo ndi Yehosafati.
Yehova, kumbukirani ana a Edomu tsiku la Yerusalemu; amene adati, Gamulani, gamulani, kufikira maziko ake.
Adzikhazikitsa mafumu a dziko lapansi, nachita upo akulu pamodzi, Kutsutsana naye Yehova, ndi Wodzozedwa wake, ndi kuti,
Ndipo Mowabu adzaonongeka asakhalenso mtundu wa anthu, chifukwa anadzikuzira yekha pa Yehova.
Ndipo anadzisonkhanitsira ana a Amoni ndi a Amaleke, namuka nakantha Israele, nalanda mzinda wa m'migwalangwa nakhalamo.