1 Mbiri 5:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo masiku a Saulo anagwirana nkhondo ndi Ahagiri, amene adagwa ndi dzanja lao; ndipo anakhala m'mahema mwao kum'mawa konse kwa Giliyadi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo masiku a Saulo anagwirana nkhondo ndi Ahagiri, amene adagwa ndi dzanja lao; ndipo anakhala m'mahema mwao kum'mawa konse kwa Giliyadi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Pa nthaŵi ya Saulo, Arubeni adathira nkhondo Ahagiri ndi kuŵagonjetsa, kenaka adakhala m'mahema mwao m'dziko lonselo kuvuma kwa Giliyadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pa nthawi ya Sauli anachita nkhondo ndi Ahagiri ndi kuwagonjetsa. Tsono iwo anakhala mʼmatenti a Ahagiri ku dera lonse la kummawa kwa Giliyadi. Onani mutuwo |