Masalimo 137:7 - Buku Lopatulika7 Yehova, kumbukirani ana a Edomu tsiku la Yerusalemu; amene adati, Gamulani, gamulani, kufikira maziko ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Yehova, kumbukirani ana a Edomu tsiku la Yerusalemu; amene adati, Gamulani, gamulani, kufikira maziko ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Kumbukirani, Inu Chauta, zimene adachita Aedomu pa tsiku lija la kuwonongeka kwa Yerusalemu, muja ankati, “Mgwetseni pansi, mgwetseni pansi, mpaka pa maziko ake.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kumbukirani, Inu Yehova, zimene Aedomu anachita pa tsiku limene Yerusalemu anagonja. Iwowo anafuwula kuti, “Mugwetseni pansi, mugwetseni pansi mpaka pa maziko ake!” Onani mutuwo |