Masalimo 137:8 - Buku Lopatulika8 Mwana wamkazi wa ku Babiloni, iwe amene udzapasulidwa; wodala iye amene adzakubwezera chilango monga umo unatichitira ife. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Mwana wamkazi wa ku Babiloni, iwe amene udzapasulidwa; wodala iye amene adzakubwezera chilango monga umo unatichitira ife. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Mzinda wa Babiloni, iwe woyenera kuwonongedwawe, adzakhala wodala munthu amene adzakubwezera zimene watichita ifezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Iwe mwana wa mkazi wa Babuloni, woyenera kuwonongedwa, wodalitsika ndi yemwe adzakubwezera pa zimene watichitira. Onani mutuwo |