Masalimo 83:7 - Buku Lopatulika7 Gebala ndi Amoni ndi Amaleke; Filistiya, pamodzi ndi iwo okhala mu Tiro. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Gebala ndi Amoni ndi Amaleke; Filistiya, pamodzi ndi iwo okhala m'Tiro. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Agebala ndi Aamoni ndi Aamaleke, Afilisti pamodzi ndi nzika za ku Tiro. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Agebala, Aamoni ndi Aamaleki, Afilisti, pamodzi ndi anthu a ku Turo. Onani mutuwo |