Masalimo 83:8 - Buku Lopatulika8 Asiriya anaphatikana nao; anakhala dzanja la ana a Loti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Asiriya anaphatikana nao; anakhala dzanja la ana a Loti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Aasiriya nawonso agwirizana nawo, kuti alimbikitse mphamvu za ana a Loti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ngakhalenso Aasiriya aphatikizana nawo kupereka mphamvu kwa ana a Loti. Sela Onani mutuwo |