Masalimo 83:9 - Buku Lopatulika9 Muwachitire monga munachitira Midiyani; ndi Sisera, ndi Yabini kumtsinje wa Kisoni, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Muwachitire monga munachitira Midiyani; ndi Sisera, ndi Yabini kumtsinje wa Kisoni, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Muŵachite zomwe mudaŵachita Amidiyani, Sisera ndi Yabini ku mtsinje wa Kisoni, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Muwachitire zomwe munachitira Amidiyani, monga munachitira Sisera ndi Yabini ku mtsinje wa Kisoni. Onani mutuwo |