Masalimo 83:10 - Buku Lopatulika10 amene anaonongeka ku Endori; anakhala ngati ndowe ya kumunda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 amene anaonongeka ku Endori; anakhala ngati ndowe ya kumunda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 amene adaŵaononga ku Endori, ndi kuŵasandutsa ndoŵe m'nthaka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Amene anawonongedwa ku Endori ndi kukhala ngati zinyalala. Onani mutuwo |