Masalimo 83:11 - Buku Lopatulika11 Muwaike akulu ao ngati Orebu ndi Zeebu; mafumu ao ngati Zeba ndi Zalimuna, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Muwaike akulu ao ngati Orebu ndi Zeebu; mafumu ao ngati Zeba ndi Zalimuna, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Akalonga ao muŵachite zomwe mudachita Orebu ndi Zeebu, ndipo ana a mafumu ao onse, muŵachite zomwe mudachita Zeba ndi Zalimuna, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Anthu awo otchuka muwachite zomwe munachita Orebu ndi Zeebu ana a mafumu muwachite zomwe munachita Zeba ndi Zalimuna, Onani mutuwo |