Masalimo 83:12 - Buku Lopatulika12 amene anati, Tilande malo okhalamo Mulungu, akhale athu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 amene anati, Tilande malo okhalamo Mulungu, akhale athu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 amene adati, “Tiyeni tilande dziko la Mulungu likhale lathu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 amene anati, “Tiyeni tilande dziko la msipu la Mulungu.” Onani mutuwo |