Fulumirani ndiyankheni, Yehova; mzimu wanga ukutha. Musandibisire nkhope yanu; ndingafanane nao akutsikira kudzenje.
Masalimo 70:1 - Buku Lopatulika Fulumirani kundipulumutsa, Mulungu! Fulumirani kundithandiza, Yehova. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Fulumirani kundipulumutsa, Mulungu! Fulumirani kundithandiza, Yehova. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Inu Mulungu, pulumutseni. Inu Chauta, fulumirani kudzandithandiza. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Fulumirani Mulungu kundipulumutsa; Yehova bwerani msanga kudzandithandiza. |
Fulumirani ndiyankheni, Yehova; mzimu wanga ukutha. Musandibisire nkhope yanu; ndingafanane nao akutsikira kudzenje.