Masalimo 71:12 - Buku Lopatulika12 Musandikhalire kutali, Mulungu; fulumirani kundithandiza, Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Musandikhalire kutali, Mulungu; fulumirani kundithandiza, Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Inu Mulungu, musandikhalire kutali. Inu Mulungu wanga, fulumirani kudzandithandiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Musakhale kutali ndi ine Inu Mulungu, bwerani msanga, Inu Mulungu wanga; thandizeni. Onani mutuwo |