Masalimo 148:5 - Buku Lopatulika Alemekeze dzina la Yehova; popeza analamulira, ndipo zinalengedwa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Alemekeze dzina la Yehova; popeza analamulira, ndipo zinalengedwa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Zonsezo zitamande dzina la Chauta! Paja Iye adaalamula, izo nkulengedwa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zonse zitamande dzina la Yehova pakuti Iye analamula ndipo zinalengedwa. |
Lemekezani Yehova, inu angelo ake; a mphamvu zolimba, akuchita mau ake, akumvera liu la mau ake.
ndiye amene amanga zipinda zake zosanja m'mwamba, nakhazika tsindwi lake padziko lapansi; Iye amene aitana madzi a m'nyanja, nawatsanulira padziko; dzina lake ndiye Yehova.
Muyenera inu, Ambuye wathu, ndi Mulungu wathu, kulandira ulemerero ndi ulemu ndi mphamvu; chifukwa mudalenga zonse, ndipo mwa chifuniro chanu zinakhala, ndipo zinalengedwa.