Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 148:6 - Buku Lopatulika

6 Anazikhazikanso kunthawi za nthawi; anazipatsa chilamulo chosatumphika.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Anazikhazikanso kunthawi za nthawi; anazipatsa chilamulo chosatumphika.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Adazikhazikitsa kuti zikhale mpaka muyaya, adaikapo lamulo limene silingathe kusinthika.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Iye anaziyika pa malo ake ku nthawi za nthawi; analamula ndipo sizidzatha.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 148:6
9 Mawu Ofanana  

Kodi udziwa malemba a kuthambo? Ukhoza kukhazikitsa ufumu wao padziko lapansi?


Udzakhazikika ngati mwezi kunthawi yonse, ndi ngati mboni yokhulupirika kuthambo.


Yehova achita ufumu; wadziveka ndi ukulu; wadziveka Yehova, wadzimangirira mphamvu m'chuuno; dziko lomwe lokhalamo anthu likhakizika, silidzagwedezeka.


Pakuti kumeneku kuli kwa Ine monga madzi a Nowa; pakuti monga ndinalumbira kuti madzi a Nowa sadzamizanso padziko lapansi, momwemo ndinalumbira kuti sindidzakukwiyira iwe, pena kukudzudzula.


Yehova atero: Likaleka kukhala pangano langa la usana ndi usiku, ngati sindinalemba malemba a kumwamba ndi dziko lapansi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa