Masalimo 148:7 - Buku Lopatulika7 Lemekezani Yehova kochokera ku dziko lapansi, zinsomba inu, ndi malo ozama onse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Lemekezani Yehova kochokera ku dziko lapansi, zinsomba inu, ndi malo ozama onse; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Tamandani Chauta inu okhala pa dziko lapansi, inu zilombo za m'madzi ndi nyanja zonse zozama, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Tamandani Yehova pa dziko lapansi, inu zolengedwa zikuluzikulu za mʼnyanja, ndi nyanja zonse zakuya, Onani mutuwo |