Masalimo 148:5 - Buku Lopatulika5 Alemekeze dzina la Yehova; popeza analamulira, ndipo zinalengedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Alemekeze dzina la Yehova; popeza analamulira, ndipo zinalengedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Zonsezo zitamande dzina la Chauta! Paja Iye adaalamula, izo nkulengedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Zonse zitamande dzina la Yehova pakuti Iye analamula ndipo zinalengedwa. Onani mutuwo |