Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 95:5 - Buku Lopatulika

5 Nyanja ndi yake, anailenga; ndipo manja ake anaumba dziko louma.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Nyanja ndi yake, anailenga; ndipo manja ake anaumba dziko louma.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Nyanja ndi yake, popeza kuti ndiye adailenga. Mtunda ndi wakenso, popeza kuti ndiye adaupanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Nyanja ndi yake, pakuti anayilenga ndi Iye, ndipo manja ake anawumba mtunda wowuma.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 95:5
9 Mawu Ofanana  

Iwowa apenya ntchito za Yehova, ndi zodabwitsa zake m'madzi ozama.


Amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zili m'mwemo. Ndiye wakusunga choonadi kosatha,


Amaunjika madzi a m'nyanja monga mulu, amakundika zakudya mosungiramo.


Asanalenge dziko, ndi thengo, ngakhale chiyambi cha fumbi la dziko.


Poikira nyanja malire ake, kuti madzi asapitirire pa lamulo lake; polemba maziko a dziko.


Kodi simundiopa Ine? Ati Yehova: simudzanthunthumira pamaso pa Ine, amene ndinaika mchenga chilekaniro cha nyanja, ndi lemba lamuyaya kuti isapitirirepo? Ndipo ngakhale mafunde ake achita gavigavi, alephera; ngakhale akokoma, sangathe kupitirirapo.


Ndipo ananena nao, Ndine Muhebri, ndiopa Yehova Mulungu wa Kumwamba, amene analenga nyanja ndi mtunda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa