A Hemani, ana a Hemani: Bukiya, Mataniya, Uziyele, Sebuele, ndi Yerimoti, Hananiya, Hanani, Eliyata, Gidaliti, ndi Romamiti-Ezere, Yosibekasa, Maloti, Hotiri, Mahaziyoti;
Numeri 3:18 - Buku Lopatulika Ndi ana a Geresoni maina ao ndi awa, monga mwa mabanja ao: Libini, ndi Simei. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndi ana a Geresoni maina ao ndi awa, monga mwa mabanja ao: Libini, ndi Simei. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono ana a Geresoni potsata mabanja ao naŵa: Labini ndi Simei. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mayina a ana a Geresoni potsata mabanja awo ndi awa: Libini ndi Simei. |
A Hemani, ana a Hemani: Bukiya, Mataniya, Uziyele, Sebuele, ndi Yerimoti, Hananiya, Hanani, Eliyata, Gidaliti, ndi Romamiti-Ezere, Yosibekasa, Maloti, Hotiri, Mahaziyoti;
Ndipo maina a ana aamuna a Levi, mwa kubadwa kwao ndiwo: Geresoni, ndi Kohati, ndi Merari; ndipo zaka za moyo wa Levi ndizo zana limodzi mphambu makumi atatu kudza zisanu ndi ziwiri.
banja la nyumba ya Levi pa lokha, ndi akazi ao pa lokha; banja la Asimei pa okha, ndi akazi ao pa okha;