Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Zekariya 12:13 - Buku Lopatulika

13 banja la nyumba ya Levi pa lokha, ndi akazi ao pa lokha; banja la Asimei pa okha, ndi akazi ao pa okha;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 banja la nyumba ya Levi pa lokha, ndi akazi ao pa lokha; banja la Asimei pa okha, ndi akazi ao pa okha;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Banja la Levi lidzalira palokha, akazi akenso adzalira paokha. Banja la Simei lidzalira palokha, akazi akenso adzalira paokha.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 nyumba ya Levi pamodzi ndi akazi awo, fuko la Simei pamodzi ndi akazi awo,

Onani mutuwo Koperani




Zekariya 12:13
16 Mawu Ofanana  

Ndipo pakufika mfumu Davide ku Bahurimu, onani, panatuluka pamenepo munthu wa banja la nyumba ya Saulo, dzina lake ndiye Simei, mwana wa Gera; iyeyu anatulukako, nayenda natukwana.


Koma Zadoki wansembe, ndi Benaya mwana wake wa Yehoyada, ndi Natani mneneri, ndi Simei, ndi Rei, ndi anthu amphamvu aja adaali ndi Davide, sanali ndi Adoniya.


Ndi ana a Simei: Yahati, Zina, ndi Yeusi, ndi Beriya. Awa anai ndiwo ana a Simei.


A Ageresoni: Ladani ndi Simei.


Ndi ana a Pedaya: Zerubabele ndi Simei; ndi ana a Zerubabele: Mesulamu, ndi Hananiya; ndipo Selomiti ndiye mlongo wao,


Ndipo Simei anali nao ana aamuna khumi mphambu asanu ndi mmodzi, ndi ana aakazi asanu ndi mmodzi; koma abale ake analibe ana ambiri, ndi banja lao lonse silinachulukitse ngati ana a Yuda.


ndi a ana a Hemani, Yehuwele ndi Simei; ndi a ana a Yedutuni, Semaya ndi Uziyele.


Ndipo dziko lidzalira, banja lililonse pa lokha; banja la nyumba ya Davide pa lokha, ndi akazi ao pa okha; banja la nyumba ya Natani pa lokha, ndi akazi ao pa okha;


mabanja onse otsala, banja lililonse pa lokha, ndi akazi ao pa okha.


Ndi ana a Geresoni maina ao ndi awa, monga mwa mabanja ao: Libini, ndi Simei.


Ndi ana a Kohati monga mwa mabanja ao: Amuramu ndi Izihara, Hebroni ndi Uziyele.


Ndi ana a Merari monga mwa mabanja ao: Mali ndi Musi. Awa ndi mabanja a Alevi monga mwa nyumba za makolo ao.


Banja la Libini, ndi mabanja a Simei, ndiwo a Geresoni; ndiwo mabanja a Geresoni.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa