Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 3:17 - Buku Lopatulika

17 Ndipo ana a Levi maina ao ndi awa: Geresoni, ndi Kohati ndi Merari.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndipo ana a Levi maina ao ndi awa: Geresoni, ndi Kohati ndi Merari.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Maina a ana a Leviwo ndi aŵa: Geresoni, Kohati ndi Merari.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Mayina a ana aamuna a Levi ndi awa: Geresoni, Kohati ndi Merari.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 3:17
12 Mawu Ofanana  

Ndi ana aamuna a Levi: Geresoni, Kohati, ndi Merari.


Ndipo Davide anawagawa magawo monga mwa ana a Levi: Geresoni, Kohati, ndi Merari.


Ndipo Mose anawawerenga monga mwa mau a Yehova, monga adamuuza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa