Numeri 3:18 - Buku Lopatulika18 Ndi ana a Geresoni maina ao ndi awa, monga mwa mabanja ao: Libini, ndi Simei. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndi ana a Geresoni maina ao ndi awa, monga mwa mabanja ao: Libini, ndi Simei. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Tsono ana a Geresoni potsata mabanja ao naŵa: Labini ndi Simei. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mayina a ana a Geresoni potsata mabanja awo ndi awa: Libini ndi Simei. Onani mutuwo |