Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 3:18 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

18 Mayina a ana a Geresoni potsata mabanja awo ndi awa: Libini ndi Simei.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

18 Ndi ana a Geresoni maina ao ndi awa, monga mwa mabanja ao: Libini, ndi Simei.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

18 Ndi ana a Geresoni maina ao ndi awa, monga mwa mabanja ao: Libini, ndi Simei.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

18 Tsono ana a Geresoni potsata mabanja ao naŵa: Labini ndi Simei.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 3:18
12 Mawu Ofanana  

Kwa Hemani, kuchokera kwa ana ake: Bukiya, Mataniya, Uzieli, Subaeli ndi Yerimoti; Hananiya, Hanani, Eliata, Gidaliti ndi Romamiti-Ezeri; Yosibakasa, Maloti, Hotiri ndi Mahazioti.


Mayina a ana a Geresomu ndi awa: Libini ndi Simei.


Mayina a ana a Levi pamodzi ndi zidzukulu zawo anali awa: Geresoni, Kohati ndi Merari. Levi anakhala ndi moyo kwa zaka 137.


nyumba ya Levi pamodzi ndi akazi awo, fuko la Simei pamodzi ndi akazi awo,


Ana a Kohati potsata mabanja awo ndi awa: Amramu, Izihari, Hebroni ndi Uzieli.


Kwa Geresoni kunali banja la Alibini, banja la Asimei. Amenewa ndiwo anali mabanja a Ageresoni.


“Werenganso Ageresoni monga mwa mabanja ndi mafuko awo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa