Numeri 3:19 - Buku Lopatulika19 Ndi ana a Kohati monga mwa mabanja ao: Amuramu ndi Izihara, Hebroni ndi Uziyele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndi ana a Kohati monga mwa mabanja ao: Amuramu ndi Izihara, Hebroni ndi Uziyele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ana a Kohati potsata mabanja ao ndi aŵa: Amuramu, Izara, Hebroni ndi Uziyele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Ana a Kohati potsata mabanja awo ndi awa: Amramu, Izihari, Hebroni ndi Uzieli. Onani mutuwo |