Numeri 4:22 - Buku Lopatulika22 Werenganso ana a Geresoni, monga mwa nyumba za makolo ao, monga mwa mabanja ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Werenganso ana a Geresoni, monga mwa nyumba za makolo ao, monga mwa mabanja ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 “Uŵerengenso ana a Geresoni potsata mabanja ao ndiponso banja la makolo ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 “Werenganso Ageresoni monga mwa mabanja ndi mafuko awo. Onani mutuwo |