Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 4:22 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 “Werenganso Ageresoni monga mwa mabanja ndi mafuko awo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

22 Werenganso ana a Geresoni, monga mwa nyumba za makolo ao, monga mwa mabanja ao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Werenganso ana a Geresoni, monga mwa nyumba za makolo ao, monga mwa mabanja ao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 “Uŵerengenso ana a Geresoni potsata mabanja ao ndiponso banja la makolo ao.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 4:22
5 Mawu Ofanana  

Mayina a ana a Geresoni potsata mabanja awo ndi awa: Libini ndi Simei.


Kwa Geresoni kunali banja la Alibini, banja la Asimei. Amenewa ndiwo anali mabanja a Ageresoni.


Mtsogoleri wa mabanja a Ageresoni anali Eliyasafu mwana wa Laeli.


Yehova anawuza Mose kuti,


Uwerenge amuna onse a zaka makumi atatu mpaka a zaka makumi asanu zakubadwa amene amabwera kudzatumikira ku tenti ya msonkhano.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa