Numeri 3:21 - Buku Lopatulika21 Banja la Libini, ndi mabanja a Simei, ndiwo a Geresoni; ndiwo mabanja a Geresoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Banja la Libini, ndi mabanja a Simei, ndiwo a Geresoni; ndiwo mabanja a Geresoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Alibini ndi Asimei anali mabanja otuluka mwa Geresoni. Ameneŵa ndiwo anali mabanja a Ageresoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Kwa Geresoni kunali banja la Alibini, banja la Asimei. Amenewa ndiwo anali mabanja a Ageresoni. Onani mutuwo |