Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 3:21 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Kwa Geresoni kunali banja la Alibini, banja la Asimei. Amenewa ndiwo anali mabanja a Ageresoni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

21 Banja la Libini, ndi mabanja a Simei, ndiwo a Geresoni; ndiwo mabanja a Geresoni.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Banja la Libini, ndi mabanja a Simei, ndiwo a Geresoni; ndiwo mabanja a Geresoni.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Alibini ndi Asimei anali mabanja otuluka mwa Geresoni. Ameneŵa ndiwo anali mabanja a Ageresoni.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 3:21
9 Mawu Ofanana  

Mayina a ana a Geresomu ndi awa: Libini ndi Simei.


Mayina a ana a Levi pamodzi ndi zidzukulu zawo anali awa: Geresoni, Kohati ndi Merari. Levi anakhala ndi moyo kwa zaka 137.


nyumba ya Levi pamodzi ndi akazi awo, fuko la Simei pamodzi ndi akazi awo,


Awanso anali mabanja a Alevi: banja la Alibini, banja la Ahebroni, banja la Amali, banja la Amusi, fuko la Kora banja la Akohati, (Kohati anali abambo a Amramu.


Mayina a ana a Geresoni potsata mabanja awo ndi awa: Libini ndi Simei.


Ana a Merari potsata mabanja awo ndi awa: Mali ndi Musi. Amenewa ndiwo anali mabanja a Alevi monga mwa makolo awo.


Chiwerengero cha amuna onse amene anawawerenga a mwezi umodzi kapena kupitirirapo chinali 7,500.


“Werenganso Ageresoni monga mwa mabanja ndi mafuko awo.


Zidzukulu za Geresoni zinapatsidwa mizinda 13 kuchokera ku mabanja a mafuko a Isakara, Aseri, Nafutali ndi theka la fuko la Manase ku Basani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa